YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE A ATUMWI 11:26

MACHITIDWE A ATUMWI 11:26 BLPB2014

ndipo m'mene anampeza, anadza naye ku Antiokeya. Ndipo kunali, kuti chaka chonse anasonkhana pamodzi mu Mpingo, naphunzitsa anthu aunyinji; ndipo ophunzira anayamba kutchedwa Akhristu ku Antiokeya.

Free Reading Plans and Devotionals related to MACHITIDWE A ATUMWI 11:26