YouVersion Logo
Search Icon

2 MBIRI 26:16

2 MBIRI 26:16 BLPB2014

Koma atakhala wamphamvu, mtima wake unakwezeka momuononga, nalakwira Yehova Mulungu wake; popeza analowa m'Kachisi wa Yehova kufukiza pa guwa la nsembe la chofukiza.