YouVersion Logo
Search Icon

1 PETRO 1:24-25

1 PETRO 1:24-25 BLPB2014

Popeza, Anthu onse akunga udzu, ndi ulemerero wao wonse ngati duwa la udzu. Udzuwo ungofota, ndi duwa lake lingogwa; koma Mau a Mulungu akhala chikhalire. Ndipo mau olalikidwa kwa inu ndi awo.

Free Reading Plans and Devotionals related to 1 PETRO 1:24-25