YouVersion Logo
Search Icon

Nyimbo ya Solomoni 8:6

Nyimbo ya Solomoni 8:6 CCL

Undiyike pamtima pako ngati chidindo, ngati chidindo cha pa dzanja lako; pakuti chikondi nʼchamphamvu ngati imfa, nsanje ndiyaliwuma ngati manda. Chikondi chimachita kuti lawilawi ngati malawi a moto wamphamvu.

Verse Image for Nyimbo ya Solomoni 8:6

Nyimbo ya Solomoni 8:6 - Undiyike pamtima pako ngati chidindo,
ngati chidindo cha pa dzanja lako;
pakuti chikondi nʼchamphamvu ngati imfa,
nsanje ndiyaliwuma ngati manda.
Chikondi chimachita kuti lawilawi
ngati malawi a moto wamphamvu.