Mateyu 5:38-39
Mateyu 5:38-39 CCL
“Munamva kuti, ‘Diso kulipira diso ndi dzino kulipira dzino.’ Koma ndikuwuzani kuti musamukanize munthu woyipa, akakumenya patsaya mupatseni tsaya linalo.