YouVersion Logo
Search Icon

Mateyu 14:18-19

Mateyu 14:18-19 CCL

Koma Iye anati, “Bweretsani kwa Ine.” Analamula anthu kuti akhale pansi pa udzu ndipo anatenga buledi musanu ndi nsomba ziwiri nayangʼana kumwamba, nayamika nagawa bulediyo. Kenaka anapereka bulediyo kwa ophunzira ake ndipo ophunzirawo anagawira anthu.

Free Reading Plans and Devotionals related to Mateyu 14:18-19