YouVersion Logo
Search Icon

Mateyu 12:34

Mateyu 12:34 CCL

Ana anjoka inu, woyipa inu, mungathe bwanji kuyankhula kanthu kalikonse kabwino? Pakuti pakamwa pamayankhula zosefuka kuchokera mu mtima.

Verse Image for Mateyu 12:34

Mateyu 12:34 - Ana anjoka inu, woyipa inu, mungathe bwanji kuyankhula kanthu kalikonse kabwino? Pakuti pakamwa pamayankhula zosefuka kuchokera mu mtima.