YouVersion Logo
Search Icon

Yeremiya 7:5-7

Yeremiya 7:5-7 CCL

Ngati mutasinthadi makhalidwe anu ndi zochita zanu, ndi kumachitirana zolungama, ngati mutaleka kuzunza mlendo, ana amasiye kapena akazi amasiye ndi kuleka kupha anthu osalakwa pa malo ano, ndipo ngati muleka kutsatira milungu ina, kuti ingakuwonongeni, Ine ndidzakulolani kukhala pa malo ano, mʼdziko limene ndinapatsa makolo anu mpaka muyaya.

Video for Yeremiya 7:5-7

Free Reading Plans and Devotionals related to Yeremiya 7:5-7