Yesaya 43:20-21
Yesaya 43:20-21 CCL
Nyama zakuthengo, nkhandwe ndi akadzidzi zinandilemekeza. Ndidzayendetsa mitsinje mʼdziko lowuma kuti ndiwapatse madzi anthu anga osankhidwa. Anthu amene ndinadziwumbira ndekha kuti aziyimba nyimbo yotamanda Ine.