YouVersion Logo
Search Icon

Yesaya 43:16-17

Yesaya 43:16-17 CCL

Yehova anapanga njira pa nyanja, anapanga njira pakati pa madzi amphamvu. Iye anasonkhanitsa magaleta, akavalo, gulu lankhondo ndi asilikali amphamvu, ndipo onse anagwa pamenepo, osadzukanso anazimitsidwa kutheratu ngati chingwe cha nyale. Yehova ameneyu akuti,