YouVersion Logo
Search Icon

Ezekieli 37:1-2

Ezekieli 37:1-2 CCL

Dzanja la Yehova linali pa ine, ndipo Mzimu wa Yehova unandinyamula nʼkukandikhazika pakati pa chigwa. Chigwacho chinali chodzaza ndi mafupa. Yehova anandiyendetsa uku ndi uku pakati pa mafupawo. Mafupawo anali ochuluka kwambiri mʼchigwa monsemo ndipo anali owuma kwambiri.

Free Reading Plans and Devotionals related to Ezekieli 37:1-2