Bible App logo
Search Icon

Ezekieli 2:2-3

Ezekieli 2:2-3 CCL

Pamene ankayankhula nane, Mzimu wa Mulungu unalowa mwa ine ndipo unandiyimiritsa, ndipo ndinamva Iye akundiyankhula. Iye anati, “Iwe mwana wa munthu, Ine ndikukutuma kwa Aisraeli, mtundu wa anthu owukira umene wandiwukira Ine; Iwo ndi makolo awo akhala akundiwukira Ine mpaka lero lino.

Free Reading Plans and Devotionals related to Ezekieli 2:2-3