YouVersion Logo
Search Icon

Eksodo 21:23-25

Eksodo 21:23-25 CCL

Koma ngati wavulazidwa kwambiri, ndiye malipiro ake adzakhala motere: moyo kulipa moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, mkono kulipa mkono, phazi kulipa phazi. Kutentha ndi moto kulipa kutentha ndi moto, bala kulipa bala, mkwingwirima kulipa mkwingwirima.