YouVersion Logo
Search Icon

Eksodo 20:9-10

Eksodo 20:9-10 CCL

Uzigwira ntchito zako zonse masiku asanu ndi limodzi. Koma tsiku lachisanu ndi chiwiri ndi Sabata, tsiku loperekedwa kwa Yehova Mulungu wako. Tsiku limeneli musagwire ntchito iliyonse, inuyo kapena mwana wanu wamwamuna kapena mwana wanu wamkazi, wantchito wanu wamwamuna kapena mdzakazi wanu, ziweto zanu kapena mlendo amene akukhala mʼmudzi mwanu.

Free Reading Plans and Devotionals related to Eksodo 20:9-10