YouVersion Logo
Search Icon

Mlaliki 3:4-5

Mlaliki 3:4-5 CCL

Nthawi yomva chisoni ndi nthawi yosangalala, nthawi yolira maliro ndi nthawi yovina. Nthawi yotaya miyala ndi nthawi yokundika miyala, nthawi yokumbatirana ndi nthawi yoleka kukumbatirana.