Mlaliki 2:24-25
Mlaliki 2:24-25 CCL
Kwa munthu palibe chabwino china kuposa kudya, kumwa ndi kukondwerera ntchito zake. Izinso ndaona kuti ndi zochokera kwa Mulungu, pakuti popanda Iye, ndani angadye ndi kupeza chisangalalo?