Danieli 5:25-28
Danieli 5:25-28 CCL
“Mawu amene analembedwa ndi awa: MENE, MENE, TEKELI, PARASINI. “Zimene mawuwa akutanthauza ndi izi: Mene: Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo wauthetsa. Tekeli: Inu mwayesedwa pa sikelo ndipo mwapezeka kuti mukuperewera. Parasini: Ufumu wanu wagawidwa ndi kupatsidwa kwa Amedi ndi Aperezi.”





