Bible App logo
Search Icon

MATEYU 21:42

MATEYU 21:42 BLP-2018

Yesu ananena kwa iwo, Kodi simunawerenge konse m'malembo, Mwala umene anaukana omanga nyumba womwewu unakhala mutu wa pangodya: Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?

Verse Image for MATEYU 21:42

MATEYU 21:42 - Yesu ananena kwa iwo, Kodi simunawerenge konse m'malembo, Mwala umene anaukana omanga nyumba womwewu unakhala mutu wa pangodya: Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?

Free Reading Plans and Devotionals related to MATEYU 21:42