YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE 26:17-18

MACHITIDWE 26:17-18 BLP-2018

ndi kukulanditsa kwa anthu, ndi kwa amitundu, amene Ine ndikutuma kwa iwo, kukawatsegulira maso ao, kuti atembenuke kuchokera kumdima, kulinga kukuunika, ndi kuchokera ulamuliro wa Satana kulinga kwa Mulungu, kuti alandire iwo chikhululukiro cha machimo, ndi cholowa mwa iwo akuyeretsedwa ndi chikhulupiriro cha mwa Ine.

Free Reading Plans and Devotionals related to MACHITIDWE 26:17-18