YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE 11:23-24

MACHITIDWE 11:23-24 BLP-2018

ameneyo, m'mene anafika, naona chisomo cha Mulungu, anakondwa; ndipo anawadandaulira onse, kuti atsimikize mtima kukhalabe ndi Ambuye; chifukwa anali munthu wabwino, ndi wodzala ndi Mzimu Woyera ndi chikhulupiriro: ndipo khamu lalikulu lidaonjezeka kwa Ambuye.

Free Reading Plans and Devotionals related to MACHITIDWE 11:23-24