1
Maluko 2:17
Nyanja
NTNYBL2025
Yesu yapo wadavela yameneyo, wadaayangha, “Wandhu yawo sadwala siafuna sing'anga, nambho anyiawo afuna sing'anga nianyiwajha adwala. Sinidajhe kwatana wandhu yawo avomelezeka pamaso pa Mnungu, nambho najha kwatana amachimo.”
Compare
Explore Maluko 2:17
2
Maluko 2:5
Yesu yapo wadaona chikhulupililo chao, wadamkambila yujha mundhu wovuwala, “Bwenji langa, nakulekelela machimo yako.”
Explore Maluko 2:5
3
Maluko 2:27
Ndiipo Yesu wadaakambila, “Siku lo Pumulila lidaikidwa ndande ya kwathangatila wandhu, ni osati kwachita wandhu akhale akapolo a siku!
Explore Maluko 2:27
4
Maluko 2:4
Saadakhoze kumpeleka pafupi ni Yesu ndande ya lijha gulu la wandhu. Chimwecho adakwela pamwamba, adafulumula chindu, pajha wadali Yesu. Yapo adafulumula, adamchicha mundhu yujha uku amgoneka pa chitala.
Explore Maluko 2:4
5
Maluko 2:10-11
Chipano, nifuna mjhiwe kuti ine Mwana wa Mundhu nali ni ulamulilo wolekelela machimo ya wandhu pajhiko.” Pamenepo, wadamkambila yujha mundhu wadavuwala, “Nikukambila, uka utenge chitala chako, upite kukhomo!”
Explore Maluko 2:10-11
6
Maluko 2:9
Nichiti chili chopepuka kupunda, kumkambila mundhu uyu wavuwala, ‘Walekeledwa machimo yako,’ kapina kumkambila, ‘Uka, utenge chitala chako upite?’
Explore Maluko 2:9
7
Maluko 2:12
Pampajha yujha wodwala wadauka, wadatenga chitala chake ni kuchoka, uku wandhu wonjhe niampenya. Wandhu wonjhe adazizwa ni kumtamanda Mnungu, niakamba, “Sitidaonepo chindhu ngati ichi.”
Explore Maluko 2:12
Home
Bible
Plans
Videos