1
Maluko 14:36
Nyanja
NTNYBL2025
Wadapembha, “Atate wanga, kwanu vindhu vonjhe vikhozekana. Mnichochele chikho ichi cha mavuto, nambho isidakhala ngati umo nifunila ine, nambho ngati umo mfunila imwe.”
Compare
Explore Maluko 14:36
2
Maluko 14:38
Ndiipo, wadaakambila, “Mchezelele ni mpembhele kuti simdayesedwa kuchita voipa. Anyiimwe mfuna kulimbila mtima mayeso nambho matupi yanu yalibe mbhavu.”
Explore Maluko 14:38
3
Maluko 14:9
Nikukambilani uzene, paliponjhe pajhiko Uthenga Wabwino yapo siilalikidwe, chindhu ichi wachichita uyu maye sichichuludwe kwa kumkumbukila Iye.”
Explore Maluko 14:9
4
Maluko 14:34
Wadaakambila, “Nili ni chisoni kupunda mumtima mwanga, chikhoza kunipha. Khalani yapa ni mchezelele.”
Explore Maluko 14:34
5
Maluko 14:22
Yapo amadya, Yesu wadatenga bumunda, wadamuyamika Munungu, wadaubandhula ni kwapacha oyaluzidwa wake uku ni wakamba, “Tengani, mudye ili ni thupi langa.”
Explore Maluko 14:22
6
Maluko 14:23-24
Ndiipo wadatenga chikho cha divai, wadamuyamika Mnungu, wadaapacha, wonjhe adachimwela. Wadaakambila, “Uwu ni mwazi wanga uwo uchimikiza chipangano cha Mnungu, mwazi uwo umwazika ndande ya wandhu ambili.
Explore Maluko 14:23-24
7
Maluko 14:27
Yapo adali mnjila Yesu wadaakambila oyaluzidwa wake, “Anyiimwe mwaonjhe simunithawe ni kunisiya ngati umo yalembedwela mmalembo Yoyela, ‘Mnungu siwambule owesa, ni mbelele zonjhe sizimwazikane.’
Explore Maluko 14:27
8
Maluko 14:42
Nyakukani! Tijhipita! Mundhu uyo siwaning'anamuke wali pampano.”
Explore Maluko 14:42
9
Maluko 14:30
Yesu wadamkambila Petulo, “Zene nikukambila, usiku wa lelo tambala wakali osalile mala kawili, siunikane mala katatu.”
Explore Maluko 14:30
Home
Bible
Plans
Videos