1
Luka 22:42
Nyanja
NTNYBL2025
“Atate, ngati ikhozekana, mavuto yaya yasadanipata, nambho osati ngati umo nifunila ine, nambho ikhale ngati umo mfunila imwe.”
Compare
Explore Luka 22:42
2
Luka 22:32
Nambho ine nakupembhelela iwe Simoni, kuti chikulupililo chako chisadachepekela, ni yapo siunibwelele waathile mtima achanjako.”
Explore Luka 22:32
3
Luka 22:19
Ndiipo, wadatenga bumunda, wadayamika, ni kuubandhula, wadapacha atumwi ni kukamba, “Ili ni thupi langa ilo lichochedwa ndande ya anyiimwe. Mjichite chimwechi ponikumbukila ine.”
Explore Luka 22:19
4
Luka 22:20
Chimwecho, yapo adamaliza kudya, wadachita chimchijha wadatenga chikho chija ni kukamba, “Divai iyi ili mchikho ni chipangano cha chipano icho chichitidwa kwa mwazi wanga, uwo umwazika ndande yanu.”
Explore Luka 22:20
5
Luka 22:44
Ni Yesu wali mkati mwa kupweteka kwakukulu, wadapembhela kupunda. Chitukuta chake chidali ngati mitondho ya mwazi iyo imasililika panjhi.
Explore Luka 22:44
6
Luka 22:26
Nambho isadakhala chimwecho kwa anyiimwe, nambho uyo wali wamkulu pakati panu ifunika wakale ngati wang'ono wa wandhu wonjhe, ni uyo walamulila wakhale ngati mbowa.
Explore Luka 22:26
7
Luka 22:34
Nambho Yesu wadamuyangha, “Nikukambila iwe Petulo, usiku wa lelo, tambala wakali osalila siukhale wanikana katatu kuti siunijhiwa.”
Explore Luka 22:34
Home
Bible
Plans
Videos