1
Luka 19:10
Nyanja
NTNYBL2025
Pakuti ine mwana wa Mundhu najha kufunafuna ni kulamicha chijha chidataika.”
Compare
Explore Luka 19:10
2
Luka 19:38
Adakamba, “Wali ni mwawi Mfumu uyo wakujha mu jhina la Ambuye. Mtendele ukhale kumwamba kwa Mnungu, ni ulemelelo kumeneko kumwamba kupunda!”
Explore Luka 19:38
3
Luka 19:9
Yesu wadamkambila, “Lelo uomboli wajha mnyumba ino, pakuti uyu nayo ni wa mwana wa mmuna wa Ibulahimu.
Explore Luka 19:9
4
Luka 19:5-6
Yesu yapo wadafika pamalo yameneyo, wadapenya mmwamba mwa mtengo ni kumkambila, “Zakayo, chika chisanga, pakuti lelo sinikhale mlendo kukhomo lako.” Zakayo wadachika chisanga ni kumlandila Yesu kwa kukondwela.
Explore Luka 19:5-6
5
Luka 19:8
Nambho Zakayo wadaima ni kwaakambila Ambuye, “Vechelani Ambuye! Ine sinaninghe wosauka chuma changa chakumojhi, ningati namlanda mundhu chindhu chalichonjhe, sinimbwezele kanayi.”
Explore Luka 19:8
6
Luka 19:39-40
Afalisayo wina yawo adali mkati mwa gulu lijha, yapo adaona chimwecho, adamkambila Yesu, “Oyaluza, anyindileni oyaluzidwa wanu akhale chete!” Yesu wadayangha, “Nikukambilani kuti, ngati anyiyawa saakhale chete, miyala siibule phokoso.”
Explore Luka 19:39-40
Home
Bible
Plans
Videos