1
Vichito 7:59-60
Nyanja
NTNYBL2025
Yapo amaendekela kumpmonya miyala, Sitifano wadapembhela, “Ambuye Yesu, landilani mzimu wanga!” Wadagwada ni kulila kwa mvekelo wa waukulu, “Ambuye, musadalamula wandhu yawa kwa machimo yaya.” Yapo wadamaliza kukamba chimwecho, wadamwalila.
Compare
Explore Vichito 7:59-60
2
Vichito 7:49
“Ambuye akamba, ‘Kumwamba ni mpando wanga wachifumu, ni pajhiko lapanjhi ni malo ya kuikapo miyendo yanga. Nyumba yamtundu wanji iyo simunimangile ine? Kapina malo yanga yopumulilamo siyakhale yati?
Explore Vichito 7:49
3
Vichito 7:57-58
Nambho anyiiwo adapunda kubula phokoso lalikulu, adacheka makutu, ndiipo wonjhe adamlumbhila kwa pamojhi. Adamtaya kubwalo kwa mujhi ni kuyamba kumponya miyala. Wajha amboni adaika njhalu zao pa miyendo ya mnyamata mmojhi uyo wamatanidwa Saulo kuti wachite ulonda.
Explore Vichito 7:57-58
Home
Bible
Plans
Videos