1
MASALIMO 96:4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Pakuti Yehova ndi wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; ayenera amuope koposa milungu yonse.
Compare
Explore MASALIMO 96:4
2
MASALIMO 96:2
Muimbireni Yehova, lemekezani dzina lake; lalikirani chipulumutso chake tsiku ndi tsiku.
Explore MASALIMO 96:2
3
MASALIMO 96:1
Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; muimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi.
Explore MASALIMO 96:1
4
MASALIMO 96:3
Fotokozerani ulemerero wake mwa amitundu; zodabwitsa zake mwa mitundu yonse ya anthu.
Explore MASALIMO 96:3
5
MASALIMO 96:9
Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa, njenjemerani pamaso pake, inu dziko lonse lapansi.
Explore MASALIMO 96:9
Home
Bible
Plans
Videos