1
YESAYA 19:25
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
pakuti Yehova wa makamu wadalitsa iwo, ndi kuti, Odalitsika Ejipito anthu anga, ndi Asiriya ntchito ya manja anga, ndi Israele cholowa changa.
Compare
Explore YESAYA 19:25
2
YESAYA 19:20
Ndipo chidzakhala chizindikiro ndi mboni ya Yehova wa makamu m'dziko la Ejipito; pakuti iwo adzalirira kwa Yehova, chifukwa cha osautsa, ndipo Iye adzawatumizira mpulumutsi, ndi wamphamvu, nadzawapulumutsa.
Explore YESAYA 19:20
3
YESAYA 19:1
Katundu wa Ejipito. Taonani, Yehova wakwera pamwamba pa mtambo wothamanga, nadza ku Ejipito; ndi mafano a Ejipito adzagwedezeka pakufika kwake, ndi mtima wa Ejipito udzasungunuka pakati pake.
Explore YESAYA 19:1
4
YESAYA 19:19
Tsiku limenelo padzakhala guwa la nsembe la Yehova pakati pa dziko la Ejipito, ndi choimiritsa cha Yehova m'malire ake.
Explore YESAYA 19:19