1
AGALATIYA 3:13
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Khristu anatiombola ku temberero la chilamulo, atakhala temberero m'malo mwathu; pakuti kwalembedwa, Wotembereredwa aliyense wopachikidwa pamtengo.
Compare
Explore AGALATIYA 3:13
2
AGALATIYA 3:28
Muno mulibe Myuda, kapena Mgriki, muno mulibe kapolo, kapena mfulu, muno mulibe mwamuna ndi mkazi; pakuti muli nonse mmodzi mwa Khristu Yesu.
Explore AGALATIYA 3:28
3
AGALATIYA 3:29
Koma ngati muli a Khristu, muli mbeu ya Abrahamu, nyumba monga mwa lonjezano.
Explore AGALATIYA 3:29
4
AGALATIYA 3:14
Kuti dalitso la Abrahamu mwa Khristu Yesu, lichitike kwa amitundu; kuti tikalandire lonjezano la Mzimuyo, mwa chikhulupiriro.
Explore AGALATIYA 3:14
5
AGALATIYA 3:11
Ndipo chidziwikatu kuti palibe munthu ayesedwa wolungama ndi lamulo pamaso pa Mulungu; pakuti, Wolungama adzakhala ndi moyo ndi chikhulupiriro
Explore AGALATIYA 3:11
Home
Bible
Plans
Videos