1
EKSODO 40:38
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Pakuti mtambo wa Yehova unakhala pa Kachisi msana, ndi usiku munali moto m'menemo, pamaso pa mbumba yonse ya Israele, m'maulendo ao onse.
Compare
Explore EKSODO 40:38
2
EKSODO 40:34-35
Pamenepo mtambo unaphimba chihema chokomanako, ndi ulemerero wa Yehova unadzaza Kachisiyo. Ndipo Mose sanathe kulowa m'chihema chokomanako, popeza mtambo unakhalabe pamenepo; ndi ulemerero wa Yehova unadzaza Kachisi.
Explore EKSODO 40:34-35
Home
Bible
Plans
Videos