1
Maliro 3:22-23
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Ife sitinawonongekeretu chifukwa chikondi cha Yehova ndi chachikulu, ndi chifundo chake ndi chosatha. Zimaoneka zatsopano mmawa uliwonse; kukhulupirika kwanu nʼkwakukulu.
Compare
Explore Maliro 3:22-23
2
Maliro 3:24
Mu mtima mwanga ndimati, “Yehova ndiye zanga zonse; motero ndimamuyembekezera.”
Explore Maliro 3:24
3
Maliro 3:25
Yehova ndi wabwino kwa amene amayembekezera Iye, kwa munthu amene amafunafuna Iyeyo
Explore Maliro 3:25
4
Maliro 3:40
Tiyeni tisanthule ndi kuyesa njira zathu, ndipo tiyeni tibwerere kwa Yehova.
Explore Maliro 3:40
5
Maliro 3:57
Munafika pafupi pamene ndinakuyitanani, ndipo munati, “Usaope.”
Explore Maliro 3:57