1
MATEYU 27:46
Buku Lopatulika
BLP-2018
Ndipo poyandikira ora lachisanu ndi chinai, Yesu anafuula ndi mau aakulu, kunena, Eli, Eli, lama sabakitani? ndiko kunena kuti, Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji Ine?
Compare
Explore MATEYU 27:46
2
MATEYU 27:51-52
Ndipo onani, chinsalu chotchinga cha mu Kachisi chinang'ambika pakati, kuchokera kumwamba kufikira pansi; ndipo dziko linagwedezeka, ndi miyala inang'ambika; ndi manda anatseguka, ndi mitembo yambiri ya anthu oyera mtima, akugona kale, inauka
Explore MATEYU 27:51-52
3
MATEYU 27:50
Ndipo Yesu, pamene anafuula ndi mau aakulu, anapereka mzimu wake.
Explore MATEYU 27:50
4
MATEYU 27:54
Ndipo anali naye akudikira Yesu, anaona chivomezi, ndi zinthu zimene zinachitidwa, anaopa kwambiri, nanena, Indedi Uyu ndiye Mwana wa Mulungu.
Explore MATEYU 27:54
5
MATEYU 27:45
Ndipo ora lachisanu ndi chimodzi panali mdima padziko lonse, kufikira ora lachisanu ndi chinai.
Explore MATEYU 27:45
6
MATEYU 27:22-23
Pilato ananena kwa iwo, Nanga ndidzachita chiyani ndi Yesu, wotchedwa Khristu? Onse anati, Apachikidwe pamtanda. Ndipo iye anati, Chifukwa ninji? Anachita choipa chotani? Koma iwo anafuulitsa kopambana, Apachikidwe pamtanda.
Explore MATEYU 27:22-23
Home
Bible
Plans
Videos