Matayo 6:25
Matayo 6:25 NTNYBL2025
“Ndendande nikukambilani msadajhichaucha pa umoyo wanu kuti simudye chiyani kapina simumwe chiyani kuti mkhale amoyo kapina mathupi yanu simuvale chiyani. Bwanji umoyo osati wa phindu kupitilila chakudya? Bwanji, thupi lilibe phindu kupitilila vivalo?