Chapa ya Youversion
Ikoni ya Utafutaji

ZEKARIYA Mau Oyamba

Mau Oyamba
Bukuli lili ndi zigawo ziwiri: Gawo loyamba ndi mau amene mneneri adalalikira kuyambira chaka cha 520 BC. Zekariya akulongosola zimene adaziwona m'masomphenya ndipo akuwachenjeza anthuwo nawalimbitsa mtima kuti akonzenso Kachisi komanso mzinda wa Yerusalemu. Iwo ayenera adziyeretsa popeza Yehova adzawadalitsa (1—8). Gawo lachiwiri ndi kaundula wa mauneneri osiyanasiyana onena za kubwera kwa Mesiya ndipo tsiku la chiweruzo (9—14).
Za mkatimu
Mau oyamba 1.1—8.23
Mau a Yehova aimba mlandu mitundu ina ya anthu 9.1-8
Mau ena olonjeza zabwino 9.9—14.21

Kuonyesha

Shirikisha

Nakili

None

Je, ungependa vivutio vyako vihifadhiwe kwenye vifaa vyako vyote? Jisajili au ingia