1
Matayo 4:4
Nyanja
NTNYBL2025
Yesu wadamuyangha, “Yalembedwa, ‘Mundhu siwakhala wa moyo kwa bumundape, Nambho kwa kila malembo yoyela yakambidwa ni Mnungu.’”
Linganisha
Chunguza Matayo 4:4
2
Matayo 4:10
Yesu wadamkambila, “Chokapo yapa iwe Woyesa! Yalembedwa mmalembo ya Mnungu, ‘Waalambile Ambuye Mnungu wako ni kwaatumikila iwo okha.’”
Chunguza Matayo 4:10
3
Matayo 4:7
Yesu wadayangha, “Chinchijha yalembedwa, ‘Usadamuyesa Ambuye Mnungu wako.’”
Chunguza Matayo 4:7
4
Matayo 4:1-2
Ndiipo Mzimu Woyela udamchogoza Yesu mbaka kuphululu kuti waesedwe ni Satana. Yesu wadamanga masiku alubaini usiku ni usana ndiipo wadavela njala.
Chunguza Matayo 4:1-2
5
Matayo 4:19-20
Yesu wadaakambila, “Majhani nichateni! Nane sinikuchiteni mukhale opeleka wandhu kwa Mnungu.” Pampajha adayasiya makoka yao niadamchata.
Chunguza Matayo 4:19-20
6
Matayo 4:17
Kuchokela nyengo imeneyo Yesu wadayamba kulalikila niwakamba, “Siyani kuchita machimo pakuti ufumu wa kumwamba wawandikila!”
Chunguza Matayo 4:17
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video