1
2 AKORINTO 4:18
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
popeza sitipenyerera zinthu zooneka, koma zinthu zosaoneka; pakuti zinthu zooneka zili za nthawi, koma zinthu zosaoneka zili zosatha.
Linganisha
Chunguza 2 AKORINTO 4:18
2
2 AKORINTO 4:16-17
Chifukwa chake sitifooka; koma ungakhale umunthu wathu wakunja uvunda, wa m'kati mwathu ukonzedwa kwatsopano tsiku ndi tsiku. Pakuti chisautso chathu chopepuka cha kanthawi chitichitira ife kulemera koposa kwakukulu ndi kosatha kwa ulemerero
Chunguza 2 AKORINTO 4:16-17
3
2 AKORINTO 4:8-9
ndife osautsika monsemo, koma osapsinjika; osinkhasinkha, koma osakhala kakasi; olondoleka, koma osatayika; ogwetsedwa, koma osaonongeka
Chunguza 2 AKORINTO 4:8-9
4
2 AKORINTO 4:7
Koma tili nacho chuma ichi m'zotengera zadothi, kuti ukulu woposa wamphamvu ukhale wa Mulungu, wosachokera kwa ife
Chunguza 2 AKORINTO 4:7
5
2 AKORINTO 4:4
mwa amene mulungu wa nthawi yino ya pansi pano unachititsa khungu maganizo ao a osakhulupirira, kuti chiwalitsiro cha Uthenga Wabwino wa ulemerero wa Khristu, amene ali chithunzithunzi cha Mulungu, chisawawalire.
Chunguza 2 AKORINTO 4:4
6
2 AKORINTO 4:6
Pakuti Mulungu amene anati, Kuunika kudzawala kutuluka mumdima, ndiye amene anawala m'mitima yathu kutipatsa chiwalitsiro cha chidziwitso cha ulemerero wa Mulungu pankhope pa Yesu Khristu.
Chunguza 2 AKORINTO 4:6
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video