1
1 AKORINTO 12:7
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Koma kwa yense kwapatsidwa maonekedwe a Mzimu kuti apindule nao.
Linganisha
Chunguza 1 AKORINTO 12:7
2
1 AKORINTO 12:27
Koma inu ndinu thupi la Khristu, ndi ziwalo, yense pa yekha.
Chunguza 1 AKORINTO 12:27
3
1 AKORINTO 12:26
Ndipo chingakhale chiwalo chimodzi chimva chowawa, ziwalo zonse zimva pamodzi; chingakhale chimodzi chilemekezedwa, ziwalo zonse zikondwera nacho pamodzi.
Chunguza 1 AKORINTO 12:26
4
1 AKORINTO 12:8-10
Pakuti kwa mmodzi kwapatsidwa mwa Mzimu mau a nzeru; koma kwa mnzake mau a chidziwitso, monga mwa Mzimu yemweyo: kwa wina chikhulupiriro, mwa Mzimu yemweyo; ndi kwa wina mphatso za machiritso, mwa Mzimu mmodziyo; ndi kwa wina machitidwe a mphamvu; ndi kwa wina chinenero; ndi kwa wina chizindikiro cha mizimu; kwa wina malilime a mitundumitundu; ndi kwa wina mamasulidwe a malilime.
Chunguza 1 AKORINTO 12:8-10
5
1 AKORINTO 12:11
Koma zonse izi achita Mzimu mmodzi yemweyo, nagawira yense pa yekha monga afuna.
Chunguza 1 AKORINTO 12:11
6
1 AKORINTO 12:25
kuti kusakhale chisiyano m'thupi; koma kuti ziwalo zifanane ndi kusamalana china ndi chinzake.
Chunguza 1 AKORINTO 12:25
7
1 AKORINTO 12:4-6
Ndipo pali mphatso zosiyana, koma Mzimu yemweyo. Ndipo pali mautumiki osiyana, koma Ambuye yemweyo. Ndipo pali machitidwe osiyana, koma Mulungu yemweyo, wakuchita zinthu zonse mwa onse.
Chunguza 1 AKORINTO 12:4-6
8
1 AKORINTO 12:28
Ndipotu Mulungu anaika ena mu Mpingo, poyamba atumwi, achiwiri aneneri, achitatu aphunzitsi, pamenepo zozizwa, pomwepo mphatso za machiritso, mathandizo, maweruziro, malilime a mitundumitundu.
Chunguza 1 AKORINTO 12:28
9
1 AKORINTO 12:14
Pakutinso thupi silikhala chiwalo chimodzi, koma zambiri.
Chunguza 1 AKORINTO 12:14
10
1 AKORINTO 12:22
Koma makamakatu ziwalozo zoyesedwa zofooka m'thupi, zifunika
Chunguza 1 AKORINTO 12:22
11
1 AKORINTO 12:17-19
Ngati thupi lonse likadakhala diso, kukadakhala kuti kununkhiza? Koma tsopano, Mulungu anaika ziwalo zonsezo m'thupi, monga anafuna. Koma ngati zonse zikadakhala chiwalo chimodzi, likadakhala kuti thupi?
Chunguza 1 AKORINTO 12:17-19
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video