1
1 AKORINTO 1:27
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
koma Mulungu anasankhula zopusa za dziko lapansi, kuti akachititse manyazi anzeru; ndipo zofooka za dziko lapansi Mulungu anazisankhula, kuti akachititse manyazi zamphamvu
Linganisha
Chunguza 1 AKORINTO 1:27
2
1 AKORINTO 1:18
Pakuti mau a mtanda ali ndithu chinthu chopusa kwa iwo akutayika, koma kwa ife amene tilikupulumutsidwa ali mphamvu ya Mulungu.
Chunguza 1 AKORINTO 1:18
3
1 AKORINTO 1:25
Chifukwa kuti chipusa cha Mulungu chiposa anthu ndi nzeru zao; ndipo chofooka cha Mulungu chiposa anthu ndi mphamvu yao.
Chunguza 1 AKORINTO 1:25
4
1 AKORINTO 1:9
Mulungu ali wokhulupirika amene munaitanidwa mwa Iye, ku chiyanjano cha Mwana wake Yesu Khristu, Ambuye wathu.
Chunguza 1 AKORINTO 1:9
5
1 AKORINTO 1:10
Koma ndikudandaulirani inu, abale, mwa dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti munene chimodzimodzi inu nonse, ndi kuti pasakhale malekano pakati pa inu; koma mumangike mu mtima womwewo ndi m'chiweruziro chomwecho.
Chunguza 1 AKORINTO 1:10
6
1 AKORINTO 1:20
Ali kuti wanzeru? Mlembi ali kuti? Ali kuti wotsutsana wa nthawi ya pansi pano? Kodi Mulungu sanaipusitsa nzeru ya dziko lapansi?
Chunguza 1 AKORINTO 1:20
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video