Chapa ya Youversion
Ikoni ya Utafutaji

YOHANE 20:21-22

YOHANE 20:21-22 BLPB2014

Chifukwa chake Yesu anatinso kwa iwo, Mtendere ukhale ndi inu; monga Atate wandituma Ine, Inenso ndituma inu. Ndipo pamene anati ichi anawapumira, nanena nao, Landirani Mzimu Woyera.