AGALATIYA 2:15-16
AGALATIYA 2:15-16 BLPB2014
Ife ndife Ayuda pachibadwidwe, ndipo sitili ochimwa a kwa amitundu; koma podziwa kuti munthu sayesedwa wolungama pa ntchito ya lamulo, koma mwa chikhulupiriro cha Yesu Khristu, ifedi tinakhulupirira kwa Khristu Yesu, kuti tikayesedwe olungama ndi chikhulupiriro cha Khristu, ndipo si ndi ntchito za lamulo; pakuti palibe munthu adzayesedwa wolungama ndi ntchito za lamulo.


