Chapa ya Youversion
Ikoni ya Utafutaji

MACHITIDWE A ATUMWI 25:6-7

MACHITIDWE A ATUMWI 25:6-7 BLPB2014

Ndipo m'mene adatsotsa mwa iwo masiku asanu ndi atatu kapena khumi okha anatsikira ku Kesareya; ndipo m'mawa mwake anakhala pa mpando wachiweruziro, nalamulira kuti atenge Paulo. Ndipo m'mene anafika iye, Ayuda adatsikawo ku Yerusalemu anaimirira pomzinga iye, namnenera zifukwa zambiri ndi zazikulu, zimene sanakhoza kuzitsimikiza

Video ya MACHITIDWE A ATUMWI 25:6-7