Chapa ya Youversion
Ikoni ya Utafutaji

MACHITIDWE A ATUMWI 1:9

MACHITIDWE A ATUMWI 1:9 BLPB2014

Ndipo m'mene adanena izi, ali chipenyerere iwo, ananyamulidwa; ndipo mtambo unamlandira Iye kumchotsa kumaso kwao.