Chapa ya Youversion
Ikoni ya Utafutaji

2 AKORINTO 5:15-16

2 AKORINTO 5:15-16 BLPB2014

ndipo adafera onse kuti iwo akukhala ndi moyo asakhalenso ndi moyo kwa iwo okha, koma mwa Iye amene adawafera iwo, nauka. Kotero kuti ife sitidziwanso munthu tsopano monga mwa thupi; ndipo ngati tazindikira Khristu monga mwa thupi, koma tsopano sitimzindikiranso motero.