1
AGALATIYA 1:10
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Pakuti kodi ndikopa anthu tsopano, kapena Mulungu? Kapena kodi ndifuna kukondweretsa anthu? Ndikadakhala wokondweretsabe anthu, sindikadakhala kapolo wa Khristu.
Linganisha
Chunguza AGALATIYA 1:10
2
AGALATIYA 1:8
Koma ngakhale ife, kapena mngelo wochokera Kumwamba, ngati akakulalikireni Uthenga Wabwino wosati umene tidakulalikirani ife, akhale wotembereredwa.
Chunguza AGALATIYA 1:8
3
AGALATIYA 1:3-4
Chisomo kwa inu, ndi mtendere wa kwa Mulungu Atate, ndi Ambuye wathu Yesu Khristu, amene anadzipereka yekha chifukwa cha machimo athu, kuti akatilanditse ife m'nyengo ya pansi pano yino yoipa, monga mwa chifuniro cha Mulungu ndi Atate wathu
Chunguza AGALATIYA 1:3-4
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video