1
AEFESO 2:10
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Pakuti ife ndife chipango chake, olengedwa mwa Khristu Yesu, kuchita ntchito zabwino, zimene Mulungu anazipangiratu, kuti tikayende m'menemo.
Linganisha
Chunguza AEFESO 2:10
2
AEFESO 2:8-9
Pakuti muli opulumutsidwa ndi chisomo chakuchita mwa chikhulupiriro, ndipo ichi chosachokera kwa inu: chili mphatso ya Mulungu; chosachokera kuntchito, kuti asadzitamandire munthu aliyense.
Chunguza AEFESO 2:8-9
3
AEFESO 2:4-5
koma Mulungu, wolemera chifundo, chifukwa cha chikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho, tingakhale tinali akufa m'zolakwa zathu, anatipatsa moyo pamodzi ndi Khristu (muli opulumutsidwa ndi chisomo)
Chunguza AEFESO 2:4-5
4
AEFESO 2:6
ndipo anatiukitsa pamodzi, natikhazikitsa pamodzi m'zakumwamba mwa Khristu Yesu
Chunguza AEFESO 2:6
5
AEFESO 2:19-20
Pamenepo ndipo simulinso alendo ndi ogonera, komatu muli a mudzi womwewo wa oyera mtima ndi a banja la Mulungu; omangika pa maziko a atumwi ndi aneneri, pali Khristu Yesu mwini, mwala wa pangodya
Chunguza AEFESO 2:19-20
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video