1
MACHITIDWE A ATUMWI 4:12
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo palibe chipulumutso mwa wina yense, pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo la kumwamba, lopatsidwa mwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.
Konpare
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 4:12
2
MACHITIDWE A ATUMWI 4:31
Ndipo m'mene adapemphera iwo, panagwedezeka pamalo pamene adasonkhanirapo; ndipo anadzazidwa onse ndi Mzimu Woyera, nalankhula mau a Mulungu molimbika mtima.
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 4:31
3
MACHITIDWE A ATUMWI 4:29
Ndipo tsopano Ambuye, penyani mau ao akuopsa, ndipo patsani kwa akapolo anu alankhule mau anu ndi kulimbika mtima konse
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 4:29
4
MACHITIDWE A ATUMWI 4:11
Iye ndiye mwalawo woyesedwa wopanda pake ndi inu omanga nyumba, umene unayesedwa mutu wa pangodya.
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 4:11
5
MACHITIDWE A ATUMWI 4:13
Koma pakuona kulimbika mtima kwa Petro ndi Yohane, ndipo pozindikira kuti ndiwo anthu osaphunzira ndi opulukira, anazizwa ndipo anawazindikira, kuti adakhala pamodzi ndi Yesu.
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 4:13
6
MACHITIDWE A ATUMWI 4:32
Ndipo unyinji wa iwo akukhulupirira anali wa mtima umodzi ndi moyo umodzi; ndipo sananena mmodzi kuti kanthu ka chuma anali nacho ndi kake ka iye yekha; koma anali nazo zonse zodyerana.
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 4:32
Akèy
Bib
Plan yo
Videyo