1
Matayo 13:23
Nyanja
NTNYBL2025
Mbeu zijha zidagwela pa ndhaka yachayila, zilingana ni mundhu uyo wavela Mawu la Mnungu, niiye wachita yayo yamkwadilicha Mnungu, ngati umo mmela umojhi uwo ubala njele miya, ni wina ubala njele sitini ni wina ubala njele selasini.”
Comparar
Explorar Matayo 13:23
2
Matayo 13:22
Mbeu ijha idavyalidwa pa minga, nde mundhu walivela mau, nambho machaucho ya jhiko ni kukhala ni khumbilo la chuma cha jhiko vilizinga mau limenelo, nisiwachita chijha Mnungu wachifuna wachichite.
Explorar Matayo 13:22
3
Matayo 13:19
Waliyonjhe wavela mawu la Ufumu wa Mnungu ni osazindikile, wali ngati mbeu zijha zidagwa mnjila, Woipa wakujha ni kulanda chijha chavyalidwa mumtima mwake.
Explorar Matayo 13:19
4
Matayo 13:20-21
Mbeu ijha idavyalidwa pa mwala ni chifani cha mundhu uyo wavela mau ni pamwepo walilandila kwa chikondwelo. Nambho walimbila mtima ndhawi yochepa, pakuti mau la Mnungu slidalowe kupunda mkati mwao. Mavuto kapina kusowedwa ndande ya mau yajha kukafika, wandhuwo abwelela mmbuyo nikugwa mtima.
Explorar Matayo 13:20-21
5
Matayo 13:44
“Ufumu wa kumwamba ulingana ni chindhu cha phindu icho chabisidwa mmunda. Mundhu mmojhi wadachivumbula, wadachibisanjho, ni kukondwela kwa kukulu uko wadali nako, wadapita kugulicha vonjhe ivo wadalinavo, ndiipo wadabwela kugula munda ujha.”
Explorar Matayo 13:44
6
Matayo 13:8
Zina zidagwela pa dothi la chaila, zidamela, ni zidakula ni kubala, imojhi idabala njele miya, ina adabala njele sitini, ni ina adabala njele selasini.”
Explorar Matayo 13:8
7
Matayo 13:30
Zisiyeni zonjhe zikulile pamojhi mbaka ndhawi yokolola. Ndhawi imeneyo sinaakambile wokolola kukusa matengo akayamange machakatamachakata ni kuyabucha. Nambho mapila kololani mkaiike mnghokwe mwanga.’”
Explorar Matayo 13:30
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos