1
Matayo 12:36-37
Nyanja
NTNYBL2025
“Zenedi Nikukambilani, siku la lamulo wandhu siafunike wakambe pa kila mawu loipa ilo alikamba. Pakuti kwa mawu yako siuvomelezeke kuti ni wabwino, ni kwa mawu yako siulamulidwe kuti ni woipa.”
Comparar
Explorar Matayo 12:36-37
2
Matayo 12:34
Anyiimwe muli woipa ngati njoka zili ni sumu! Mkhoza bwanji kukamba vindhu vabwino ikakhala mwachinawene wake woipa? Pakuti mundhu wakamba yajha yajhala mumtima mwake.
Explorar Matayo 12:34
3
Matayo 12:35
Mundhu wabwino wachocha vindhu vabwino vali mumtima mwake ni mundhu woipa wachocha vindhu voyipa vali mumtima mwake.”
Explorar Matayo 12:35
4
Matayo 12:31
Chimwecho nikukambilani, volakwa vonjhe ni chipongwe avichita wandhu saalekeleledwe, nambho yao amchitala chipongwe Mzimu Woyela saalekeleledwa machimo yao.
Explorar Matayo 12:31
5
Matayo 12:33
“Mtengo wabwino ubala vipacho vabwino, ni mtengo waopa ubala vipacho voipa. Pakuti mtengo ujhiwika pa vipacho vake.
Explorar Matayo 12:33
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos