Genesis 49:22-23

Genesis 49:22-23 CCL

“Yosefe ali ngati mtengo wobereka zipatso, mtengo wobereka zipatso pafupi ndi kasupe, nthambi zake zimayanga pa chipupa cha mwala. Alenje a uta anamuchita chiwembu mwankhanza; anamuthamangitsa ndi mauta awo.