1
Matayo 9:37-38
Nyanja
NTNYBL2025
Pamenepo wadaakambila oyaluzidwa wake, “Vokolola ni vambili, nambho wandhu wochita njhito ni wochepa. Mwaapembhe Ambuye Mnungu mwene vokolola apeleke ochita njhito mmunda mwake.”
比較
Matayo 9:37-38で検索
2
Matayo 9:13
Nambho mpite mkajhiyaluze mate ya mawu yaya, Nifuna lisungu, osati njhembe. Sinidajhe kwatana wandhu abwino nambho amachimo.”
Matayo 9:13で検索
3
Matayo 9:36
Yesu yapo wadaona wandhu magulu kwa magulu, wadalengela lisungu ndande adali ni mandha ni adamwazika ngati mbelele zilibe owesa.
Matayo 9:36で検索
4
Matayo 9:12
Yesu yapo wadavela yameneyo, wadakamba, “Wandhu yawo asangalala siafuna singanga nambho odwala.
Matayo 9:12で検索
5
Matayo 9:35
Yesu wamaendaenda mmijhi ni mvijhijhi, wamayaluza mnyumba zao zokomanilana Ayahudi ni wadaalalikila Uthenga Wabwino wa ufumu wa Mnungu, ni kulamicha matenda ni mavuto yonjhe.
Matayo 9:35で検索
ホーム
聖書
読書プラン
ビデオ