1
Matayo 15:18-19
Nyanja
NTNYBL2025
Nambho chindhu icho chituluka mkamwa chichoka mumtima, chimenecho nde icho chimchita mundhu siwadavomelezeka pakumlambila Mnungu. Pakuti mumtima yachoka maganizo ya kupha, chigololo, uhule, unami, kuba, umboni wanthila ni matukwano.
Konpare
Eksplore Matayo 15:18-19
2
Matayo 15:11
Osati chijha chimlowa mkamwa nde icho chimchita mundhu siwadavomelezeka kwa kumlambila Mnungu, nambho chijha chimchoka mundhu nde icho chimchita siwadavomelezeka pakumlambila Mnungu.”
Eksplore Matayo 15:11
3
Matayo 15:8-9
‘Mnungu wakamba kuti wandhu anyiyawa anilemekeza kwa maupe, nambho mmitima mwao alipatali ni ine. Kunilambila kwao kulibe mate, pakuti ayaluza mayaluzo ya wandhu ngati mayaluzo yanga!’”
Eksplore Matayo 15:8-9
4
Matayo 15:28
Ndiipo Yesu wadamuyangha, “Wamkazi iwe, chikhulupi chako chachikulu, siuchitilidwe icho udachipembha.” Pampajha mwali wake wadalama.
Eksplore Matayo 15:28
5
Matayo 15:25-27
Wamkazi yujha wadajha ni kumgwadila Yesu, niwapembha, “Pepani Ambuye mnithangatile.” Yesu wadayangha, “Osati bwino kutenga chakudya cha wana ni kwaaponyela agalu.” Wamkazi yujha wadayangha, “Yetu Ambuye, nambho ata agalu akudya vakudya ivo vikugwa panjhi mbuye wake yapo wakudya.”
Eksplore Matayo 15:25-27
Akèy
Bib
Plan yo
Videyo